Mateyu 21:23 BL92

23 Ndipo m'mene Iye analowa m'Kacisi, ansembe akuru ndi akuru anthu anadza kwa Iye analikuphunzitsa, nanena, Mucita izi ndi ulamuliro wotani? Ndipo ndani anakupatsani ulamuliro wotere?

Werengani mutu wathunthu Mateyu 21

Onani Mateyu 21:23 nkhani