38 Koma olimawo m'mene anaona mwanayo, ananena wina ndi mnzace, Uyo ndiye wolowa; tiyeni, timuphe, ndipo ife tidzatenga colowa cace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 21
Onani Mateyu 21:38 nkhani