41 Iwo ananena kwa Iye, Adzaononga koipa oipawo, nadzapereka mundawo kwa olima ena, amene adzambwezera iye zipatso pa nyengo zace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 21
Onani Mateyu 21:41 nkhani