45 Ndipo ansembe akuru ndi Afarisi, pakumva mafanizo ace, anazindikira kuti alikunena za iwo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 21
Onani Mateyu 21:45 nkhani