Mateyu 22:10 BL92

10 Ndipo akapolo ao anaturukira kunjira, nasonkhanitsa onse amene anawapeza, ngakhale oipa, ngakhale abwino; ndipo ukwatiwo unadzala ndi okhala pacakudya.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 22

Onani Mateyu 22:10 nkhani