21 Nanena iwo, Ca Kaisara. Pomwepo Iye anati kwa iwo, Cifukwa cace patsani kwa Kaisara zace za Kaisara, ndi kwa Mulungu zace za Mulungu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 22
Onani Mateyu 22:21 nkhani