Mateyu 22:28 BL92

28 Cifukwa cace m'kuuka kwa akufa, iye adzakhala mkazi wa yani wa asanu ndi awiriwo? pakuti onse anakhala naye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 22

Onani Mateyu 22:28 nkhani