12 Ndipo amene ali yense akadzikuza yekha adzacepetsedwa; koma amene adzicepetsa mwini yekha adzakulitsidwa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 23
Onani Mateyu 23:12 nkhani