22 Ndipo wakulumbira kuchula Kumwamba, alumbira cimpando ca Mulungu, ndi Iye wakukhala pomwepo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 23
Onani Mateyu 23:22 nkhani