29 Tsoka inu, alembi ndi Afarisi, onyenga! cifukwa mumanga nyumba za pa manda a aneneri, ndipo mukonza manda a anthu olungama,
Werengani mutu wathunthu Mateyu 23
Onani Mateyu 23:29 nkhani