Mateyu 23:3 BL92

3 cifukwa cace zinthu ziri zonse zimene iwo akauza inu, citani nimusunge; koma musatsanza nchito zao; pakuti iwo amalankhula, komasamacita.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 23

Onani Mateyu 23:3 nkhani