39 Pakuti ndinena kwa inu, Simudzandionanso Ine, kuyambira tsopano, kufikira mudzanena,Wolemekezedwa Iye amene akudza m'dzina la Ambuye.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 23
Onani Mateyu 23:39 nkhani