22 Ndipo akadaleka kufupikitsidwa masiku awo, sakadapulumuka munthu ali yense: koma cifukwa ca osankhidwawo masiku awo adzafupikitsidwa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 24
Onani Mateyu 24:22 nkhani