27 Pakuti monga mphezi idzera kum'mawa, nionekera kufikira kumadzulo; kotero kudzakhalanso kufika kwace kwa Mwana wa munthu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 24
Onani Mateyu 24:27 nkhani