39 ndipo iwo sanadziwa kanthu, kufikira kumene cigumula cinadza, cinapululutsa iwo onse, kotero kudzakhala kufika kwace kwa Mwana wa munthu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 24
Onani Mateyu 24:39 nkhani