Mateyu 24:6 BL92

6 Koma inu mudzayamba kumva za nkhondo, ndi mbiri za nkhondo; onani, musadere nkhawa; pakuti kuyenera kuti izi zioneke; koma citsiriziro sicinafike.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 24

Onani Mateyu 24:6 nkhani