9 Pamenepo adzakuperekani kunsautso, nadzakuphani; ndipo anthu a mitundu yonse adzadana nanu, cifukwa ca dzina langa.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 24
Onani Mateyu 24:9 nkhani