Mateyu 25:1 BL92

1 Pomwepo Ufumu wa Kumwamba udzafanizidwa ndi anamwali khumi, amene anatenga nyali zao, naturuka kukakomana ndi mkwati.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 25

Onani Mateyu 25:1 nkhani