10 Ndipo pamene iwo analikumuka kukagula, mkwati anafika; ndipo okonzekawo, analowa naye pamodzi muukwati; ndipo anatseka pakhomo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:10 nkhani