Mateyu 25:15 BL92

15 Ndipo mmodzi anampatsa ndalama za matalente zisanu, ndi wina ziwiri, ndi wina imodzi; kwa iwo onse monga nzeru zao; namuka iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 25

Onani Mateyu 25:15 nkhani