Mateyu 25:18 BL92

18 Koma uyo amene analandira imodziyo anamuka, nakumba pansi, naibisa ndalama ya mbuye wace.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 25

Onani Mateyu 25:18 nkhani