22 Ndipo wa ndalama ziwiriyo anadzanso, nati, Mbuye, munandipatsa ine ndalama ziwiri; onani, ndapindulapo ndalama zina ziwiri.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:22 nkhani