26 Koma mbuye wace anayankha, nati kwa iye, Kapolo iwe woipa ndi waulesi, unadziwa kuti ndimatuta kumene sindinafesa, ndi kusonkhanitsa kumene sindinawaza;
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:26 nkhani