Mateyu 25:35 BL92

35 pakuti ndinali ndi njala, ndipo munandipatsa Ine kudya; ndinali ndi ludzu, ndipo munandimwetsa Ine; ndinali mlendo, ndipo munacereza Ine;

Werengani mutu wathunthu Mateyu 25

Onani Mateyu 25:35 nkhani