41 Pomwepo Iye adzanena kwa iwo a ku dzanja lamanzere, Cokani kwa Ine otembereredwa inu, ku mota wa nthawi zonse wokolezedwera mdierekezi ndi amithenga ace:
Werengani mutu wathunthu Mateyu 25
Onani Mateyu 25:41 nkhani