13 Indetu ndinena kwa inu, kumene kuli konse uthenga uwu wabwino udzalalikidwa m'dziko lonse lapansi, ici cimene mkaziyo anacitaci cidzakambidwanso cikumbukiro cace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:13 nkhani