18 Nati Iye, Mukani kumzinda kwa munthu wangana, mukati kwa iye, Mphunzitsi anena. Nthawi yanga yayandikirai ndidzadya Paskha kwanu pamodzi ndi ophunzira anga.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:18 nkhani