Mateyu 26:31 BL92

31 Pamenepo Yesu ananena kwa iwo, Inu nonse mudzakhumudwa cifukwa ca Ine usiku uno; pakuti kwalembedwa,Ndidzakantha mbusa,Ndipo zidzabalalikaNkhosa za gulu.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 26

Onani Mateyu 26:31 nkhani