39 Ndipo anamuka patsogolo pang'ono, nagwa nkhope yace pansi, napemphera, nati, Atate, ngati nkutheka, cikho ici cindipitirire Ine; koma si monga ndifuna Ine, koma lou.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:39 nkhani