65 Pomwepo mkuru wa ansembe 6 anang'amba zobvala zace, nati, Acitira Mulungu mwano; tifuniranji mboni zina? onani, tsopano mwamva mwanowo;
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:65 nkhani