71 Ndipo pamene iye anaturuka kunka kucipata, mkazi wina anamuona, nati kwa iwo a pomwepo, Uyonso anali ndi Yesu Mnazarayo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 26
Onani Mateyu 26:71 nkhani