17 Cifukwa cace pamene anasonkhana, Pilato ananena kwa iwo, Mufuna kuti ndikumasulireni yani? Baraba kodi, kapena Yesu, wochedwa Kristu?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 27
Onani Mateyu 27:17 nkhani