31 Ndipo pamene anatha kumcitira Iye cipongwe, anabvula malaya aja, nambveka Iye malaya ace, namtsogoza Iye kukampacika pamtanda.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 27
Onani Mateyu 27:31 nkhani