Mateyu 27:48 BL92

48 Ndipo pomwepa mmodzi wa iwo anathamanga, 8 natenga cinkhupule, nacidzaza ndi vinyo wosasa, naciika pabango, namwetsa Iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 27

Onani Mateyu 27:48 nkhani