53 ndipo anaturuka m'manda mwao pambuyo pa kuuka kwace, nalowa m'mzinda woyera, naonekera kwa anthu ambiri.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 27
Onani Mateyu 27:53 nkhani