Mateyu 28:10 BL92

10 Pomwepo Yesu ananena kwa iwo, Musaope; pitani, kauzeni abale anga kuti amuke ku Galileya, ndipo adzandiona Ine kumeneko.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 28

Onani Mateyu 28:10 nkhani