Mateyu 28:15 BL92

15 Ndipo iwo analandira ndalamazo, nacita monga anawalangiza: ndipo mbiri iyo inabuka mwa Ayuda, kufikira lero lomwe.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 28

Onani Mateyu 28:15 nkhani