20 ndi kuwaphunzitsa, asunge zinthu zonse zimene ndinakulamulirani inu; ndipo onani, Ine ndiri pamodzi ndi inu masiku onse, kufikira cimariziro ca nthawi ya pansi pano.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 28
Onani Mateyu 28:20 nkhani