12 couluzira cace ciri m'dzanja lace, ndipo adzayeretsa padwale pace; ndipo adzasonkhanitsa tirigu wace m'ciruli, koma mankhusu adzatentha ndi moto wosazima.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 3
Onani Mateyu 3:12 nkhani