Mateyu 3:15 BL92

15 Koma Yesu anayankha, nati kwa iye, Balola tsopano: pakuti kuyenera ife kukwaniritsa cilungamo conse motero. Pamenepo anamlola Iye.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 3

Onani Mateyu 3:15 nkhani