4 Ndipo Yohane yekhayo anali naco cobvala cace ca ubweya wangamila, ndi lamba lacikopa m'cuuno mwace; ndi cakudya cace cinali dzombe ndi uci wa kuthengo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 3
Onani Mateyu 3:4 nkhani