9 ndipo musamayesa kunena mwa inu nokha, Atate wathu tiri naye Abrahamu; pakuti ndinena kwa inu kuti mwa miyala iyi Mulungu akhoza kuukitsira Abrahamu ana.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 3
Onani Mateyu 3:9 nkhani