10 Pomwepo Yesu ananena kwa iye, Coka Satana, pakuti kwalembedwa,Ambuye Mulungu wako udzamgwadira,Ndipo Iye yekha yekha udzamlambira.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 4
Onani Mateyu 4:10 nkhani