23 Ndipo Yesu anayendayenda m'Galileya monse, analikuphunzitsa m'masunagoge mwao, nalalikira uthenga wabwino wa Ufumu, naciritsa nthenda zonse ndi kudwala konse mwa anthu.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 4
Onani Mateyu 4:23 nkhani