Mateyu 4:4 BL92

4 Koma Iye anayankha nati, Kwalembedwa,Munthu sadzakhala ndi moyo ndi mkate wokha, koma ndi mau onse akuturuka m'kamwa mwa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 4

Onani Mateyu 4:4 nkhani