28 koma Ine ndinena kwa inu, kuti yense wakuyang'ana mkazi kumkhumba, pamenepo watha kucita naye cigololo mumtima mwace.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 5
Onani Mateyu 5:28 nkhani