32 koma Ine ndinena kwa inu, kuti 4 yense wakucotsa mkazi wace, kosati cifukwa ca cigololo, amcititsa cigololo: ndipo amene adzakwata wocotsedwayo acita cigololo.
Werengani mutu wathunthu Mateyu 5
Onani Mateyu 5:32 nkhani