Mateyu 5:40 BL92

40 Ndipo kwa iye wofuna kupita nawe kumlandu ndi kutenga malaya ako, umlolezenso copfunda cako.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 5

Onani Mateyu 5:40 nkhani