Mateyu 5:45 BL92

45 kotero kuti mukakhale ana a Atate wanu wa Kumwamba; cifukwa Iye amakwezera dzuwa lace pa oipa ndi pa abwino, namabvumbitsira mvula pa olungama ndi pa osalungama.

Werengani mutu wathunthu Mateyu 5

Onani Mateyu 5:45 nkhani