47 Ndipo ngati mulankhula abale anu okha okha, mucitanji coposa ena? Kodi angakhale anthu akunja sacita comweco?
Werengani mutu wathunthu Mateyu 5
Onani Mateyu 5:47 nkhani